Yoswa 10:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Yoswa anawapha kuchokera ku Kadesi-barinea+ mpaka ku Gaza+ ndi dera lonse la Goseni+ mpaka ku Gibeoni.+ Yoswa 15:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Goseni,+ Holoni, ndi Gilo.+ Mizinda 11 ndi midzi yake.
41 Yoswa anawapha kuchokera ku Kadesi-barinea+ mpaka ku Gaza+ ndi dera lonse la Goseni+ mpaka ku Gibeoni.+