Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 34:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Malirewo akadutse kum’mwera kwa chitunda cha Akirabimu+ kulowera ku Zini, n’kuloweranso kum’mwera kwa Kadesi-barinea.+ Kenako akakhotere ku Hazara-adara+ n’kukafika ku Azimoni.

  • Deuteronomo 9:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Yehova atakutumani kuchokera ku Kadesi-barinea+ kuti, ‘Kwerani ndi kukatenga dziko limene ndidzakupatsani kuti likhale lanu,’ pamenepo munapandukiranso malamulo a Yehova Mulungu wanu,+ ndipo simunasonyeze chikhulupiriro+ mwa iye komanso simunamvere mawu ake.+

  • Yoswa 15:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Malirewo analowera kum’mwera kuchitunda cha Akirabimu+ n’kukafika ku Zini.+ Kenako anakwera kuchokera kum’mwera kupita ku Kadesi-barinea,+ n’kukadutsa ku Hezironi mpaka ku Adara, n’kuzungulira kukafika ku Karika.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena