Numeri 13:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Iwo anabwera kwa Mose ndi Aroni, ndiponso kwa khamu lonse la ana a Isiraeli m’chipululu cha Parana, ku Kadesi.+ Anafotokozera onsewo za ulendo wawo n’kuwaonetsa zipatso za kudzikolo. Numeri 32:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 N’zimenenso makolo anu anachita+ ku Kadesi-barinea,+ pamene ndinawatuma kuti akazonde dziko.
26 Iwo anabwera kwa Mose ndi Aroni, ndiponso kwa khamu lonse la ana a Isiraeli m’chipululu cha Parana, ku Kadesi.+ Anafotokozera onsewo za ulendo wawo n’kuwaonetsa zipatso za kudzikolo.