Numeri 13:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Koma amuna amene anapita naye limodzi ananena kuti: “Sitingathe kukalimbana nawo anthuwo, chifukwa ndi amphamvu kuposa ifeyo.”+ Yoswa 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthu amene ndinapita nawo, anapangitsa mitima ya anthu kuchita mantha kwambiri.+ Koma ine ndinatsatira Yehova Mulungu wanga ndi mtima wonse.+
31 Koma amuna amene anapita naye limodzi ananena kuti: “Sitingathe kukalimbana nawo anthuwo, chifukwa ndi amphamvu kuposa ifeyo.”+
8 Anthu amene ndinapita nawo, anapangitsa mitima ya anthu kuchita mantha kwambiri.+ Koma ine ndinatsatira Yehova Mulungu wanga ndi mtima wonse.+