Numeri 32:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iwo atafika kuchigwa* cha Esikolo+ n’kuliona dzikolo, anatayitsa mtima ana a Isiraeli, kuti asakalowe m’dziko limene Yehova anatsimikiza mtima kuwapatsa.+ Deuteronomo 1:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Tipite kuti? Abale athu achititsa mantha mitima yathu+ potiuza kuti: “Kumeneko tinaonako anthu akuluakulu, ndiponso aatali kuposa ifeyo,+ ndi mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri yofika kumwamba.+ Kumeneko tinaonakonso ana a Anaki.”’+ Yoswa 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthu amene ndinapita nawo, anapangitsa mitima ya anthu kuchita mantha kwambiri.+ Koma ine ndinatsatira Yehova Mulungu wanga ndi mtima wonse.+
9 Iwo atafika kuchigwa* cha Esikolo+ n’kuliona dzikolo, anatayitsa mtima ana a Isiraeli, kuti asakalowe m’dziko limene Yehova anatsimikiza mtima kuwapatsa.+
28 Tipite kuti? Abale athu achititsa mantha mitima yathu+ potiuza kuti: “Kumeneko tinaonako anthu akuluakulu, ndiponso aatali kuposa ifeyo,+ ndi mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri yofika kumwamba.+ Kumeneko tinaonakonso ana a Anaki.”’+
8 Anthu amene ndinapita nawo, anapangitsa mitima ya anthu kuchita mantha kwambiri.+ Koma ine ndinatsatira Yehova Mulungu wanga ndi mtima wonse.+