Numeri 13:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndipo iwo anapitiriza kuuza ana a Isiraeliwo zoipa+ za dziko limene anakalizondalo, kuti: “Dziko limene tinakalizondalo limameza anthu ake, ndipo anthu onse amene tinawaona kumeneko ndi ziphona zamatupi akuluakulu.+ Deuteronomo 1:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma inu simunafune kupita kukalowa m’dzikolo,+ ndipo munayamba kupandukira lamulo la Yehova Mulungu wanu.+
32 Ndipo iwo anapitiriza kuuza ana a Isiraeliwo zoipa+ za dziko limene anakalizondalo, kuti: “Dziko limene tinakalizondalo limameza anthu ake, ndipo anthu onse amene tinawaona kumeneko ndi ziphona zamatupi akuluakulu.+
26 Koma inu simunafune kupita kukalowa m’dzikolo,+ ndipo munayamba kupandukira lamulo la Yehova Mulungu wanu.+