Numeri 14:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Komanso amuna amene Mose anawatuma kukazonda dzikolo, amene atabwerako anapangitsa anthu onse kudandaula motsutsana ndi Mose, mwa kunena zoipa zokhudza dzikolo,+ Numeri 32:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iwo atafika kuchigwa* cha Esikolo+ n’kuliona dzikolo, anatayitsa mtima ana a Isiraeli, kuti asakalowe m’dziko limene Yehova anatsimikiza mtima kuwapatsa.+
36 Komanso amuna amene Mose anawatuma kukazonda dzikolo, amene atabwerako anapangitsa anthu onse kudandaula motsutsana ndi Mose, mwa kunena zoipa zokhudza dzikolo,+
9 Iwo atafika kuchigwa* cha Esikolo+ n’kuliona dzikolo, anatayitsa mtima ana a Isiraeli, kuti asakalowe m’dziko limene Yehova anatsimikiza mtima kuwapatsa.+