Amosi 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “‘Koma ine ndinawononga Aamori+ chifukwa cha anthu anga. Aamoriwo misinkhu yawo inali yofanana ndi mitengo ya mkungudza ndipo mphamvu zawo zinali zofanana ndi za mitengo ikuluikulu.+ Ndinawononga zipatso zawo m’mwamba ndiponso mizu yawo pansi.+
9 “‘Koma ine ndinawononga Aamori+ chifukwa cha anthu anga. Aamoriwo misinkhu yawo inali yofanana ndi mitengo ya mkungudza ndipo mphamvu zawo zinali zofanana ndi za mitengo ikuluikulu.+ Ndinawononga zipatso zawo m’mwamba ndiponso mizu yawo pansi.+