Numeri 14:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma mtumiki wanga Kalebe,+ chifukwa wasonyeza kuti ali ndi mzimu wosiyana ndi wa ena, ndipo wakhala akunditsatira ndi mtima wonse,+ ndithudi ndidzam’lowetsa m’dziko limene anakalizonda, ndipo mbadwa zake zidzakhalamo ngati dziko lawo.+ Numeri 32:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma Kalebe+ mwana wa Yefune Mkenizi, ndi Yoswa+ mwana wa Nuni, adzaiona nthakayo chifukwa akhala akumvera Yehova ndi mtima wonse.’
24 Koma mtumiki wanga Kalebe,+ chifukwa wasonyeza kuti ali ndi mzimu wosiyana ndi wa ena, ndipo wakhala akunditsatira ndi mtima wonse,+ ndithudi ndidzam’lowetsa m’dziko limene anakalizonda, ndipo mbadwa zake zidzakhalamo ngati dziko lawo.+
12 Koma Kalebe+ mwana wa Yefune Mkenizi, ndi Yoswa+ mwana wa Nuni, adzaiona nthakayo chifukwa akhala akumvera Yehova ndi mtima wonse.’