-
Yoswa 19:49Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
49 Apa m’pamene anamalizira kugawa dzikolo m’zigawozigawo kuti akhalemo. Kenako ana a Isiraeli anam’patsa cholowa Yoswa mwana wa Nuni pakati pawo.
-