Yoswa 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndinali ndi zaka 40 pamene Mose mtumiki wa Yehova anandituma kukazonda dziko,+ kuchokera ku Kadesi-barinea. Nditabwerako ndinamuuza kuchokera pansi pa mtima wanga, zonse zimene ndinaona.+
7 Ndinali ndi zaka 40 pamene Mose mtumiki wa Yehova anandituma kukazonda dziko,+ kuchokera ku Kadesi-barinea. Nditabwerako ndinamuuza kuchokera pansi pa mtima wanga, zonse zimene ndinaona.+