Numeri 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Utume amuna kuti akazonde dziko la Kanani limene ndikulipereka kwa ana a Isiraeli.+ Pa fuko lililonse utume mwamuna mmodzi, amene ali mtsogoleri+ wa fukolo.” Numeri 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Wa fuko la Yuda anali Kalebe,+ mwana wa Yefune. Ezekieli 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pa tsiku limenelo ndinakweza dzanja langa+ powalumbirira kuti ndidzawatulutsa m’dziko la Iguputo kupita nawo kudziko limene ndinaliyendera kuti iwo akakhalemo, dziko loyenda mkaka ndi uchi.+ Linali dziko lokongola kwambiri kuposa mayiko onse.+
2 “Utume amuna kuti akazonde dziko la Kanani limene ndikulipereka kwa ana a Isiraeli.+ Pa fuko lililonse utume mwamuna mmodzi, amene ali mtsogoleri+ wa fukolo.”
6 Pa tsiku limenelo ndinakweza dzanja langa+ powalumbirira kuti ndidzawatulutsa m’dziko la Iguputo kupita nawo kudziko limene ndinaliyendera kuti iwo akakhalemo, dziko loyenda mkaka ndi uchi.+ Linali dziko lokongola kwambiri kuposa mayiko onse.+