Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 48:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Phiri la Ziyoni limene lili m’dera lakutali la kumpoto,+

      Ndi lokongola chifukwa lili pamalo okwezeka ndi osangalatsa padziko lonse lapansi,+

      Mudzi wa Mfumu Yaikulu.+

  • Danieli 8:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Imodzi mwa nyangazi inatulutsa nyanga ina yaing’ono+ imene inayamba kukula kwambiri moloza kum’mwera, moloza kotulukira dzuwa ndiponso moloza ku Dziko Lokongola.+

  • Danieli 11:41
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 41 Iyo idzalowanso+ m’Dziko Lokongola+ ndipo idzachititsa mayiko ambiri kupunthwa,+ koma Edomu, Mowabu+ ndi mbali yaikulu ya ana a Amoni adzapulumuka m’manja mwake.

  • Zekariya 7:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 ‘Chotero ndinawabalalitsira ku mitundu yonse ya anthu+ imene sanali kuidziwa,+ ngati kuti atengedwa ndi mphepo yamkuntho. Dzikoli analisiya labwinja, popanda munthu wodutsamo kapena kuyendayendamo.+ Iwo anasandutsa dziko losiririka+ kukhala chinthu chodabwitsa.’”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena