Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 48:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Phiri la Ziyoni limene lili m’dera lakutali la kumpoto,+

      Ndi lokongola chifukwa lili pamalo okwezeka ndi osangalatsa padziko lonse lapansi,+

      Mudzi wa Mfumu Yaikulu.+

  • Ezekieli 20:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pa tsiku limenelo ndinakweza dzanja langa+ powalumbirira kuti ndidzawatulutsa m’dziko la Iguputo kupita nawo kudziko limene ndinaliyendera kuti iwo akakhalemo, dziko loyenda mkaka ndi uchi.+ Linali dziko lokongola kwambiri kuposa mayiko onse.+

  • Danieli 8:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Imodzi mwa nyangazi inatulutsa nyanga ina yaing’ono+ imene inayamba kukula kwambiri moloza kum’mwera, moloza kotulukira dzuwa ndiponso moloza ku Dziko Lokongola.+

  • Danieli 11:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Mfumu yobwera kudzamenyana nayo* idzachita zofuna zake, ndipo palibe adzaime pamaso pake. Mfumuyo idzaimirira m’Dziko Lokongola,+ ndipo idzapha anthu ambiri.+

  • Danieli 11:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 Ndipo idzamanga mahema okhala ngati nyumba yachifumu pakati pa nyanja yaikulu ndi phiri lopatulika la Dziko Lokongola.+ Ndiyeno iyo idzafika kumapeto a moyo wake+ ndipo sipadzapezeka woithandiza.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena