Ezekieli 38:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Udzanena kuti: “Ndipita kukaukira dziko lokhala ndi midzi yopanda mipanda.+ Ndipita kukaukira anthu amene akukhala mwabata, popanda chowasokoneza. Ndikaukira anthu onsewo amene akukhala m’midzi yopanda mipanda+ ndipo alibe zotsekera ndiponso zitseko.” Ezekieli 38:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “‘Pa tsiku limenelo, tsiku limene Gogi adzabwere m’dziko la Isiraeli, mkwiyo wanga udzatulukira m’mphuno mwanga,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.+
11 Udzanena kuti: “Ndipita kukaukira dziko lokhala ndi midzi yopanda mipanda.+ Ndipita kukaukira anthu amene akukhala mwabata, popanda chowasokoneza. Ndikaukira anthu onsewo amene akukhala m’midzi yopanda mipanda+ ndipo alibe zotsekera ndiponso zitseko.”
18 “‘Pa tsiku limenelo, tsiku limene Gogi adzabwere m’dziko la Isiraeli, mkwiyo wanga udzatulukira m’mphuno mwanga,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.+