Yesaya 26:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 M’tsiku limenelo,+ m’dziko la Yuda+ mudzaimbidwa nyimbo+ yakuti: “Ife tili ndi mzinda wolimba.+ Iye waika chipulumutso ngati mipanda ndiponso ngati chiunda chomenyerapo nkhondo.*+ Zekariya 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mngeloyo anauza mnzakeyo kuti: “Thamanga ukauze mnyamata uyo kuti, ‘“Mu Yerusalemu mudzakhala anthu ngati mudzi wopanda mpanda+ chifukwa cha kuchuluka kwa anthu ndi ziweto zimene zili mmenemo.+
26 M’tsiku limenelo,+ m’dziko la Yuda+ mudzaimbidwa nyimbo+ yakuti: “Ife tili ndi mzinda wolimba.+ Iye waika chipulumutso ngati mipanda ndiponso ngati chiunda chomenyerapo nkhondo.*+
4 Mngeloyo anauza mnzakeyo kuti: “Thamanga ukauze mnyamata uyo kuti, ‘“Mu Yerusalemu mudzakhala anthu ngati mudzi wopanda mpanda+ chifukwa cha kuchuluka kwa anthu ndi ziweto zimene zili mmenemo.+