Ekisodo 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mdaniyo anati, ‘Ndiwathamangira,+ ndi kuwapeza!+Ndigawa chuma chawo.+ Pamenepo moyo wanga ukhutira ndi zimene ndawachita!Ndisolola lupanga langa! Dzanja langa liwawononga!’+ Yeremiya 49:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Nyamukani, amuna inu. Pitani kukaukira mtundu wa anthu umene ukukhala mosatekeseka+ ndi mwamtendere!”+ watero Yehova. “Kumeneko kulibe zitseko ndi mipiringidzo. Anthu ake amakhala kwaokhaokha.+
9 Mdaniyo anati, ‘Ndiwathamangira,+ ndi kuwapeza!+Ndigawa chuma chawo.+ Pamenepo moyo wanga ukhutira ndi zimene ndawachita!Ndisolola lupanga langa! Dzanja langa liwawononga!’+
31 “Nyamukani, amuna inu. Pitani kukaukira mtundu wa anthu umene ukukhala mosatekeseka+ ndi mwamtendere!”+ watero Yehova. “Kumeneko kulibe zitseko ndi mipiringidzo. Anthu ake amakhala kwaokhaokha.+