Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 23:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Pakuti pomwe ndili pano ndikutha kuwaona, pamwamba pa matanthwe pano,

      Ndikuwaona ndithu, pano pamwamba pa mapiri.

      Akukhala paokhaokha m’mahema awo,+

      Iwo akudziona kuti ndi osiyana ndi mitundu ina.+

  • Deuteronomo 33:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Isiraeli adzakhala motetezeka,+

      Kasupe wa Yakobo adzakhala mosatekeseka,+

      M’dziko lokhala ndi chakudya ndi vinyo watsopano.+

      Ndipo kumwamba kwake kudzagwetsa mame.+

  • Mika 7:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Weta anthu ako ndi ndodo yako.+ Weta gulu la nkhosa zomwe ndi cholowa chako, zimene zinali kukhala zokhazokha m’nkhalango pakati pa mitengo ya zipatso.+ Uzilole kuti zikadyere ku Basana ndi ku Giliyadi+ ngati mmene zinali kuchitira masiku akale.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena