Yeremiya 50:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Isiraeli ndidzamubwezeretsa kumalo ake odyerako msipu+ moti adzadya msipu paphiri la Karimeli+ ndi ku Basana.+ Iye adzakhutira m’madera amapiri a Efuraimu+ ndi Giliyadi.’”+ Ezekieli 34:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndidzazipatsa m’busa mmodzi,+ amene ndi mtumiki wanga Davide,+ ndipo adzazidyetsa. Iye adzakhala m’busa wawo ndipo adzazidyetsadi.+
19 Isiraeli ndidzamubwezeretsa kumalo ake odyerako msipu+ moti adzadya msipu paphiri la Karimeli+ ndi ku Basana.+ Iye adzakhutira m’madera amapiri a Efuraimu+ ndi Giliyadi.’”+
23 Ndidzazipatsa m’busa mmodzi,+ amene ndi mtumiki wanga Davide,+ ndipo adzazidyetsa. Iye adzakhala m’busa wawo ndipo adzazidyetsadi.+