Yeremiya 50:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Isiraeli ndidzamubwezeretsa kumalo ake odyerako msipu+ moti adzadya msipu paphiri la Karimeli ndi ku Basana.+ Ndipo iye adzakhutira mʼmapiri a Efuraimu+ ndi Giliyadi.’”+
19 Isiraeli ndidzamubwezeretsa kumalo ake odyerako msipu+ moti adzadya msipu paphiri la Karimeli ndi ku Basana.+ Ndipo iye adzakhutira mʼmapiri a Efuraimu+ ndi Giliyadi.’”+