Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 11:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Padzakhala msewu waukulu+ wochokera kudziko la Asuri woti mudzadutse anthu ake amene adzatsale,+

      Ngati mmene zinalili kwa Aisiraeli pamene ankatuluka mʼdziko la Iguputo.

  • Yesaya 65:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Sharoni+ adzakhala malo odyetserako nkhosa

      Ndipo chigwa cha Akori+ chidzakhala malo opumulirapo ngʼombe,

      Anthu anga amene akundifunafuna ndidzawachitira zimenezi.

  • Yeremiya 23:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Kenako ndidzasonkhanitsa pamodzi nkhosa zanga zotsala kuchokera mʼmayiko onse kumene ndinazibalalitsira+ ndipo ndidzazibwezeretsa kumalo awo kumene zimadyera.+ Nkhosazo zidzaberekana ndi kuchuluka.+

  • Yeremiya 33:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Anthu a mu Yuda ndi a mu Isiraeli amene anatengedwa kupita kudziko lina ndidzawabwezeretsa+ ndipo adzakhalanso ngati mmene analili poyamba.+

  • Ezekieli 34:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Nkhosazo ndidzazidyetsera mʼmalo a msipu wabwino ndipo malo amene zizidzadya msipu adzakhala kumapiri ataliatali a ku Isiraeli.+ Kumeneko zizidzagona pansi mʼmalo abwino kwambiri odyetserako ziweto+ ndipo zizidzadya msipu wabwino kwambiri mʼmapiri a ku Isiraeli.

  • Mika 2:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndithu ndidzasonkhanitsa mbadwa zonse za Yakobo.

      Ndidzasonkhanitsa Aisiraeli otsala.+

      Ndidzawabweretsa pamalo amodzi ngati gulu la nkhosa mʼkhola,

      Komanso ngati gulu la ziweto pamalo amsipu.+

      Kumeneko kudzakhala phokoso la anthu.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena