Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 11:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pa tsiku limenelo Yehova adzaperekanso dzanja lake kachiwiri kuti atenge anthu ake otsala kuchokera ku Asuri,+ ku Iguputo,+ ku Patirosi,+ ku Kusi,+ ku Elamu,+ ku Sinara,* ku Hamati ndi mʼzilumba zamʼnyanja.+

  • Yesaya 35:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Anthu amene Yehova anawawombola adzabwerera+ ndipo adzafika ku Ziyoni akufuula mosangalala.+

      Chisangalalo chosatha chidzakhala ngati chisoti chachifumu kumutu kwawo.+

      Adzakhala okondwa ndi osangalala

      Ndipo chisoni ndi kubuula zidzachoka.+

  • Yeremiya 29:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndidzakulolani kuti mundipeze,’+ akutero Yehova. ‘Ndidzasonkhanitsa anthu amene anagwidwa nʼkutengedwa kupita kumayiko ena kuchokera mʼmitundu yonse ndi kumalo onse kumene ndinakubalalitsirani,’+ akutero Yehova. ‘Kenako ndidzakubwezeretsani kumalo amene ndinakuchotsani pa nthawi imene ndinakupititsani ku ukapolo.’+

  • Yeremiya 31:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Ine ndikuwabweretsa kuchokera kudziko lakumpoto,+

      Ndidzawasonkhanitsa pamodzi kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+

      Pakati pawo padzakhala anthu amene ali ndi vuto losaona, olumala,+

      Azimayi oyembekezera komanso amene atsala pangʼono kubereka,

      Onse pamodzi adzabwerera kuno ali chigulu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena