Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 50:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Isiraeli ndidzamubwezeretsa kumalo ake odyerako msipu+ moti adzadya msipu paphiri la Karimeli ndi ku Basana.+ Ndipo iye adzakhutira mʼmapiri a Efuraimu+ ndi Giliyadi.’”+

  • Ezekieli 34:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Nkhosazo ndidzazidyetsera mʼmalo a msipu wabwino ndipo malo amene zizidzadya msipu adzakhala kumapiri ataliatali a ku Isiraeli.+ Kumeneko zizidzagona pansi mʼmalo abwino kwambiri odyetserako ziweto+ ndipo zizidzadya msipu wabwino kwambiri mʼmapiri a ku Isiraeli.

  • Mika 2:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndithu ndidzasonkhanitsa mbadwa zonse za Yakobo.

      Ndidzasonkhanitsa Aisiraeli otsala.+

      Ndidzawabweretsa pamalo amodzi ngati gulu la nkhosa mʼkhola,

      Komanso ngati gulu la ziweto pamalo amsipu.+

      Kumeneko kudzakhala phokoso la anthu.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena