Obadiya 19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iwo adzatenga dera la Negebu kukhala lawo, komanso adzatenga dera lamapiri la Esau,+ dera la Sefela ndi dera la Afilisiti.+ Iwo adzatenganso madera a Efuraimu+ ndi Samariya kukhala awo.+ Benjamini adzatenga dera la Giliyadi+ kukhala lake.
19 Iwo adzatenga dera la Negebu kukhala lawo, komanso adzatenga dera lamapiri la Esau,+ dera la Sefela ndi dera la Afilisiti.+ Iwo adzatenganso madera a Efuraimu+ ndi Samariya kukhala awo.+ Benjamini adzatenga dera la Giliyadi+ kukhala lake.