Yesaya 11:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo adzauluka paphewa la Afilisiti kumadzulo,+ ndipo onsewa pamodzi, adzalanda katundu wa ana aamuna a Kum’mawa.+ Adzatambasulira dzanja lawo pa Edomu ndi Mowabu,+ ndipo ana a Amoni adzawagonjera.+ Amosi 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndidzachita zimenezi kuti anthu anga adzatenge zinthu zotsala za Edomu+ ndi mitundu yonse ya anthu imene inali kuitanira pa dzina langa,’+ watero Yehova, amene akuchita zimenezi.
14 Iwo adzauluka paphewa la Afilisiti kumadzulo,+ ndipo onsewa pamodzi, adzalanda katundu wa ana aamuna a Kum’mawa.+ Adzatambasulira dzanja lawo pa Edomu ndi Mowabu,+ ndipo ana a Amoni adzawagonjera.+
12 Ndidzachita zimenezi kuti anthu anga adzatenge zinthu zotsala za Edomu+ ndi mitundu yonse ya anthu imene inali kuitanira pa dzina langa,’+ watero Yehova, amene akuchita zimenezi.