Yesaya 47:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano imva izi iwe mkazi wokonda zosangalatsa, wokhala pabwino,+ iwe amene umanena mumtima mwako kuti: “Ndine ndekha, palibenso wina.+ Sindidzakhala wamasiye ndipo ana anga sadzafa.”+
8 Tsopano imva izi iwe mkazi wokonda zosangalatsa, wokhala pabwino,+ iwe amene umanena mumtima mwako kuti: “Ndine ndekha, palibenso wina.+ Sindidzakhala wamasiye ndipo ana anga sadzafa.”+