Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Danieli 5:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndiyeno mfumu Belisazara+ anakonzera nduna zake 1,000 phwando lalikulu, ndipo iyeyo anali kumwa vinyo+ atakhala kutsogolo kwawo.

  • Danieli 5:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Mwadzikweza pamaso pa Ambuye wakumwamba+ ndipo anthu akubweretserani ziwiya za m’nyumba yake.+ Inuyo, nduna zanu, adzakazi anu ndi akazi anu ena apambali mwamwera vinyo m’ziwiya zimenezi. Mwatamanda milungu wamba yasiliva, yagolide, yamkuwa, yachitsulo, yamitengo ndi yamiyala+ imene siona, kumva kapena kudziwa kalikonse.+ Koma Mulungu amene amasunga mpweya wanu+ ndi njira zanu zonse m’dzanja lake,+ simunamulemekeze.+

  • Chivumbulutso 18:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Iye wamwetsa mitundu yonse ya anthu+ vinyo wa mkwiyo, vinyo wa dama lake. Ndipo mafumu a dziko lapansi anachita naye dama.+ Amalonda oyendayenda+ a padziko lapansi analemera chifukwa cha zinthu zambiri zamtengo wapatali zimene mkazi ameneyu anadziunjikira mopanda manyazi.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena