Miyambo 20:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mayendedwe a mwamuna wamphamvu amachokera kwa Yehova,+ koma kodi munthu wochokera kufumbi angazindikire bwanji njira yake?+ Yeremiya 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ine ndikudziwa bwino, inu Yehova, kuti munthu wochokera kufumbi alibe ulamuliro wowongolera njira ya moyo wake. Munthu amene akuyenda alibe ulamuliro wowongolera mapazi ake.+
24 Mayendedwe a mwamuna wamphamvu amachokera kwa Yehova,+ koma kodi munthu wochokera kufumbi angazindikire bwanji njira yake?+
23 Ine ndikudziwa bwino, inu Yehova, kuti munthu wochokera kufumbi alibe ulamuliro wowongolera njira ya moyo wake. Munthu amene akuyenda alibe ulamuliro wowongolera mapazi ake.+