Yesaya 37:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kodi ndani amene iwe wamutonza+ ndi kumulankhula monyoza?+Ndipo ndani amene iwe wam’kwezera mawu,+Ndi kum’kwezera maso ako m’mwamba?+Ndi Woyera wa Isiraeli!+ Yeremiya 50:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Babulo muitanireni oponya mivi ndi uta, onse okunga uta.+ Mangani misasa momuzungulira. Pasapezeke wothawa.+ Mubwezereni zimene anachita.+ Muchitireni zonse zimene iye anachita.+ Iye wachita zinthu modzikuza pamaso pa Yehova, pamaso pa Woyera wa Isiraeli.+
23 Kodi ndani amene iwe wamutonza+ ndi kumulankhula monyoza?+Ndipo ndani amene iwe wam’kwezera mawu,+Ndi kum’kwezera maso ako m’mwamba?+Ndi Woyera wa Isiraeli!+
29 “Babulo muitanireni oponya mivi ndi uta, onse okunga uta.+ Mangani misasa momuzungulira. Pasapezeke wothawa.+ Mubwezereni zimene anachita.+ Muchitireni zonse zimene iye anachita.+ Iye wachita zinthu modzikuza pamaso pa Yehova, pamaso pa Woyera wa Isiraeli.+