Yesaya 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yalani patebulo. Ikani mipando m’malo mwake. Idyani, imwani.+ Akalonga inu,+ nyamukani, dzozani chishango.+ Yeremiya 51:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 “Chilakolako chawo chikadzakhala champhavu kwambiri ndidzawakonzera mapwando ndipo ndidzawaledzeretsa kuti asangalale.+ Pamenepo adzagona tulo tomwe tidzakhalapo mpaka kalekale, ndipo sadzadzukanso,”+ watero Yehova.
5 Yalani patebulo. Ikani mipando m’malo mwake. Idyani, imwani.+ Akalonga inu,+ nyamukani, dzozani chishango.+
39 “Chilakolako chawo chikadzakhala champhavu kwambiri ndidzawakonzera mapwando ndipo ndidzawaledzeretsa kuti asangalale.+ Pamenepo adzagona tulo tomwe tidzakhalapo mpaka kalekale, ndipo sadzadzukanso,”+ watero Yehova.