Yesaya 22:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Komatu anthuwo adzakondwera ndi kusangalala. Adzapha ng’ombe ndi nkhosa. Adzadya nyama ndi kumwa vinyo.+ Iwo adzati, ‘Tiyeni tidye ndi kumwa, pakuti mawa tifa.’”+ Danieli 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno mfumu Belisazara+ anakonzera nduna zake 1,000 phwando lalikulu, ndipo iyeyo anali kumwa vinyo+ atakhala kutsogolo kwawo.
13 Komatu anthuwo adzakondwera ndi kusangalala. Adzapha ng’ombe ndi nkhosa. Adzadya nyama ndi kumwa vinyo.+ Iwo adzati, ‘Tiyeni tidye ndi kumwa, pakuti mawa tifa.’”+
5 Ndiyeno mfumu Belisazara+ anakonzera nduna zake 1,000 phwando lalikulu, ndipo iyeyo anali kumwa vinyo+ atakhala kutsogolo kwawo.