Yesaya 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yalani patebulo. Ikani mipando m’malo mwake. Idyani, imwani.+ Akalonga inu,+ nyamukani, dzozani chishango.+ 1 Akorinto 15:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ngati ndinamenyana ndi zilombo ku Efeso+ monga ena anachitira, ndinapindulapo chiyani? Ngati akufa sadzauka, “tiyeni tidye ndi kumwa, pakuti mawa tifa.”+ Yakobo 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mwalidyerera dziko lapansi ndipo mwasangalala.+ Mwanenepetsa mitima yanu pa tsiku lokaphedwa.+
5 Yalani patebulo. Ikani mipando m’malo mwake. Idyani, imwani.+ Akalonga inu,+ nyamukani, dzozani chishango.+
32 Ngati ndinamenyana ndi zilombo ku Efeso+ monga ena anachitira, ndinapindulapo chiyani? Ngati akufa sadzauka, “tiyeni tidye ndi kumwa, pakuti mawa tifa.”+