Yeremiya 50:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 “Lupanga lidzawononga Akasidi,”+ watero Yehova, “lidzawononganso anthu okhala m’Babulo,+ akalonga ake+ ndi anthu ake anzeru.+ Yeremiya 51:57 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Ndidzaledzeretsa akalonga, anthu ake anzeru, abwanamkubwa ake, atsogoleri ake ndi anthu ake amphamvu.+ Adzagona tulo tomwe tidzakhalapo mpaka kalekale ndipo sadzadzukanso,”+ yatero Mfumu,+ imene dzina lake ndi Yehova wa makamu.+
35 “Lupanga lidzawononga Akasidi,”+ watero Yehova, “lidzawononganso anthu okhala m’Babulo,+ akalonga ake+ ndi anthu ake anzeru.+
57 Ndidzaledzeretsa akalonga, anthu ake anzeru, abwanamkubwa ake, atsogoleri ake ndi anthu ake amphamvu.+ Adzagona tulo tomwe tidzakhalapo mpaka kalekale ndipo sadzadzukanso,”+ yatero Mfumu,+ imene dzina lake ndi Yehova wa makamu.+