Yeremiya 51:57 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Ndidzaledzeretsa akalonga, anthu ake anzeru, abwanamkubwa ake, atsogoleri ake ndi anthu ake amphamvu.+ Adzagona tulo tomwe tidzakhalapo mpaka kalekale ndipo sadzadzukanso,”+ yatero Mfumu,+ imene dzina lake ndi Yehova wa makamu.+
57 Ndidzaledzeretsa akalonga, anthu ake anzeru, abwanamkubwa ake, atsogoleri ake ndi anthu ake amphamvu.+ Adzagona tulo tomwe tidzakhalapo mpaka kalekale ndipo sadzadzukanso,”+ yatero Mfumu,+ imene dzina lake ndi Yehova wa makamu.+