2 Akorinto 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Abale, sitikufuna kuti mukhale osadziwa za masautso amene tinakumana nawo m’chigawo cha Asia,+ pamene tinali pa vuto lalikulu lotiposa mphamvu, moti tinalibenso chiyembekezo choti tikhala ndi moyo.+
8 Abale, sitikufuna kuti mukhale osadziwa za masautso amene tinakumana nawo m’chigawo cha Asia,+ pamene tinali pa vuto lalikulu lotiposa mphamvu, moti tinalibenso chiyembekezo choti tikhala ndi moyo.+