Machitidwe 19:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pa nthawi yomweyo panabuka chisokonezo chachikulu+ chokhudzana ndi Njirayo.+ 1 Akorinto 15:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ngati ndinamenyana ndi zilombo ku Efeso+ monga ena anachitira, ndinapindulapo chiyani? Ngati akufa sadzauka, “tiyeni tidye ndi kumwa, pakuti mawa tifa.”+ 1 Akorinto 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 pakuti khomo lalikulu la mwayi wautumiki landitsegukira,+ koma pali otsutsa ambiri. 2 Akorinto 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndi atumiki a Khristu kapena? Ndikuyankha ngati wamisala, ineyo ndiye weniweni woposanso iwowo:+ m’ntchito zovuta mowirikiza koposa,+ m’ndende osachita kunena,+ kumenyedwa kosawerengeka, kutsala pang’ono kufa kawirikawiri.+
32 Ngati ndinamenyana ndi zilombo ku Efeso+ monga ena anachitira, ndinapindulapo chiyani? Ngati akufa sadzauka, “tiyeni tidye ndi kumwa, pakuti mawa tifa.”+
23 Ndi atumiki a Khristu kapena? Ndikuyankha ngati wamisala, ineyo ndiye weniweni woposanso iwowo:+ m’ntchito zovuta mowirikiza koposa,+ m’ndende osachita kunena,+ kumenyedwa kosawerengeka, kutsala pang’ono kufa kawirikawiri.+