Machitidwe 19:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Choncho ku Makedoniya anatumizako awiri mwa anthu amene anali kumutumikira, omwe ndi Timoteyo+ ndi Erasito.+ Koma iye anatsalira m’chigawo cha Asia kwa kanthawi ndithu. Machitidwe 20:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Akuluwo atafika, iye anawauza kuti: “Inu mukudziwa bwino mmene ndinali kukhalira nanu nthawi zonse kuchokera tsiku loyamba limene ndinaponda m’chigawo cha Asia.+
22 Choncho ku Makedoniya anatumizako awiri mwa anthu amene anali kumutumikira, omwe ndi Timoteyo+ ndi Erasito.+ Koma iye anatsalira m’chigawo cha Asia kwa kanthawi ndithu.
18 Akuluwo atafika, iye anawauza kuti: “Inu mukudziwa bwino mmene ndinali kukhalira nanu nthawi zonse kuchokera tsiku loyamba limene ndinaponda m’chigawo cha Asia.+