Machitidwe 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako iwo anapita ku Fulugiya ndiponso m’dziko la Galatiya,+ chifukwa mzimu woyera unawaletsa kulankhula mawu opatulika m’chigawo cha Asia. Machitidwe 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Izi zinachitika kwa zaka ziwiri,+ moti onse okhala m’chigawo cha Asia,+ Ayuda ndi Agiriki omwe, anamva mawu a Ambuye.
6 Kenako iwo anapita ku Fulugiya ndiponso m’dziko la Galatiya,+ chifukwa mzimu woyera unawaletsa kulankhula mawu opatulika m’chigawo cha Asia.
10 Izi zinachitika kwa zaka ziwiri,+ moti onse okhala m’chigawo cha Asia,+ Ayuda ndi Agiriki omwe, anamva mawu a Ambuye.