Machitidwe 20:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Akuluwo atafika, iye anawauza kuti: “Inu mukudziwa bwino mmene ndinali kukhalira nanu nthawi zonse kuchokera tsiku loyamba limene ndinaponda m’chigawo cha Asia.+ 2 Timoteyo 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iwe ukudziwa kuti anthu onse m’chigawo cha Asia+ andisiya.+ Ena mwa iwo ndi Fugelo ndi Heremogene.
18 Akuluwo atafika, iye anawauza kuti: “Inu mukudziwa bwino mmene ndinali kukhalira nanu nthawi zonse kuchokera tsiku loyamba limene ndinaponda m’chigawo cha Asia.+
15 Iwe ukudziwa kuti anthu onse m’chigawo cha Asia+ andisiya.+ Ena mwa iwo ndi Fugelo ndi Heremogene.