Danieli 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chotero Mfumu Belisazara inachita mantha kwambiri ndipo nkhope yake inasintha. Nduna zakenso zinathedwa nzeru.+ Danieli 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 M’chaka choyamba cha ulamuliro wa Belisazara+ mfumu ya Babulo, Danieli analota maloto ndipo anaona masomphenya atagona pabedi lake.+ Pa nthawi imeneyo, analemba zimene analotazo,+ ndipo anafotokoza nkhani yonseyo. Danieli 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 M’chaka chachitatu cha ulamuliro wa mfumu Belisazara,+ ineyo Danieli ndinaona masomphenya pambuyo pa masomphenya amene ndinaona poyambirira aja.+
9 Chotero Mfumu Belisazara inachita mantha kwambiri ndipo nkhope yake inasintha. Nduna zakenso zinathedwa nzeru.+
7 M’chaka choyamba cha ulamuliro wa Belisazara+ mfumu ya Babulo, Danieli analota maloto ndipo anaona masomphenya atagona pabedi lake.+ Pa nthawi imeneyo, analemba zimene analotazo,+ ndipo anafotokoza nkhani yonseyo.
8 M’chaka chachitatu cha ulamuliro wa mfumu Belisazara,+ ineyo Danieli ndinaona masomphenya pambuyo pa masomphenya amene ndinaona poyambirira aja.+