Numeri 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye anawauza kuti: “Mvetserani mawu anga. Pakanakhala mneneri wa Yehova pakati panu, ndikanamudziwitsa za ine m’masomphenya,+ ndipo ndikanalankhula naye m’maloto.+ Yobu 33:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye amawalankhula m’maloto+ ndi m’masomphenya+ a usiku,Anthu akakhala m’tulo tofa nato,Akamagona pabedi.+ Yeremiya 23:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mneneri amene walota maloto anene maloto akewo. Koma amene ndamuuza mawu anga, alankhule mawu angawo moona.”+ “Kodi mapesi a tirigu angafanane ndi tirigu weniweniyo?”+ watero Yehova. Danieli 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno usiku, chinsinsicho chinaululidwa kwa Danieli m’masomphenya.+ Pamenepo Danieli anatamanda+ Mulungu wakumwamba. Danieli 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 M’chaka chachitatu cha ulamuliro wa mfumu Belisazara,+ ineyo Danieli ndinaona masomphenya pambuyo pa masomphenya amene ndinaona poyambirira aja.+
6 Iye anawauza kuti: “Mvetserani mawu anga. Pakanakhala mneneri wa Yehova pakati panu, ndikanamudziwitsa za ine m’masomphenya,+ ndipo ndikanalankhula naye m’maloto.+
15 Iye amawalankhula m’maloto+ ndi m’masomphenya+ a usiku,Anthu akakhala m’tulo tofa nato,Akamagona pabedi.+
28 Mneneri amene walota maloto anene maloto akewo. Koma amene ndamuuza mawu anga, alankhule mawu angawo moona.”+ “Kodi mapesi a tirigu angafanane ndi tirigu weniweniyo?”+ watero Yehova.
19 Ndiyeno usiku, chinsinsicho chinaululidwa kwa Danieli m’masomphenya.+ Pamenepo Danieli anatamanda+ Mulungu wakumwamba.
8 M’chaka chachitatu cha ulamuliro wa mfumu Belisazara,+ ineyo Danieli ndinaona masomphenya pambuyo pa masomphenya amene ndinaona poyambirira aja.+