Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 41:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Udzapeta+ mapiri ndi zitundazo ndipo mphepo idzaziuluza.+ Mphepo yamkuntho idzaziuluzira kumalo osiyanasiyana.+ Iweyo udzasangalala chifukwa cha Yehova.+ Udzadzitama chifukwa cha Woyera wa Isiraeli.”+

  • Luka 3:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Fosholo yake youluzira mankhusu* ili m’manja mwake. Akufuna kuyeretseratu mbee! malo ake opunthirapo mbewu ndi kututira+ tirigu munkhokwe yake. Koma mankhusu+ adzawatentha ndi moto+ umene sungazimitsidwe.”

  • 1 Akorinto 3:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 ntchito ya wina aliyense idzaonekera. Pakuti tsikulo lidzasonyeza ntchitoyo poyera, chifukwa moto ndiwo udzaonetsa zimenezo poyera,+ ndipo motowo udzaonetsa kuti ntchito ya munthu aliyense ndi yotani.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena