Yeremiya 27:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho mitundu yonse ya anthu idzatumikira iyeyo,+ mwana wake wamwamuna ndi mdzukulu wake mpaka idzafike nthawi yoti ufumu wake uthe.+ Pamenepo, mitundu yambiri ya anthu ndi mafumu amphamvu adzamugwiritsa ntchito ngati wantchito wawo.’+ Danieli 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno mfumu Belisazara+ anakonzera nduna zake 1,000 phwando lalikulu, ndipo iyeyo anali kumwa vinyo+ atakhala kutsogolo kwawo. Danieli 5:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Usiku womwewo, Belisazara mfumu ya Akasidi anaphedwa,+
7 Choncho mitundu yonse ya anthu idzatumikira iyeyo,+ mwana wake wamwamuna ndi mdzukulu wake mpaka idzafike nthawi yoti ufumu wake uthe.+ Pamenepo, mitundu yambiri ya anthu ndi mafumu amphamvu adzamugwiritsa ntchito ngati wantchito wawo.’+
5 Ndiyeno mfumu Belisazara+ anakonzera nduna zake 1,000 phwando lalikulu, ndipo iyeyo anali kumwa vinyo+ atakhala kutsogolo kwawo.