Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 137:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Iwe mwana wamkazi wa Babulo, amene udzafunkhidwa,+

      Wodala ndi amene adzakubwezera+

      Zimene iwe watichitira.+

  • Yeremiya 25:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “‘Ndiyeno zaka 70 zimenezo zikadzakwanira,+ ndidzabwezera mfumu ya Babulo ndi mtundu umenewo zolakwa zawo.+ Ndidzabwezera zolakwa za dziko la Akasidi+ ndipo dziko lawolo lidzakhala mabwinja mpaka kalekale,’+ watero Yehova.

  • Yeremiya 50:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “Zungulirani Babulo ndi kumuukira kuchokera kumbali zonse,+ inu nonse odziwa kukunga uta.+ Mulaseni+ ndipo musasunge muvi uliwonse, pakuti iye wachimwira Yehova.+

  • Yeremiya 50:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Iphani ng’ombe zake zonse zazing’ono zamphongo.+ Zonse zipite kokaphedwa.+ Tsoka kwa iwo, chifukwa tsiku lawo lafika. Nthawi yoti alangidwe yafika.+

  • Danieli 5:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 “Kumasulira kwa mawuwa ndi uku: MENE, Mulungu wawerenga masiku a ufumu wanu ndipo waumaliza.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena