Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 23:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Choncho, njira zawo zidzawakhalira ngati malo oterera+ amdima ndipo adzawakankhira m’njirazo moti adzagwa.”+

      “Pakuti ndidzawagwetsera tsoka, tsiku la chilango chawo lidzafika,”+ watero Yehova.

  • Yeremiya 48:44
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 44 ‘Aliyense wothawa chifukwa cha mantha adzagwera m’dzenje. Aliyense wotuluka m’dzenjemo adzagwidwa mumsampha.’+

      “‘Pakuti ine ndidzachititsa kuti chaka chopereka chilango kwa anthu a ku Mowabu chifike,’+ watero Yehova.

  • Yeremiya 51:52
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 52 “Chotero masiku adzafika,” watero Yehova, “ndipo ndidzalanga zifaniziro zake zogoba.+ M’dziko lake lonse anthu obayidwa adzakhala akubuula.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena