Yesaya 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Aliyense amene adzapezedwe adzabooledwa ndipo aliyense amene adzagwidwe limodzi ndi anthu ena onse pa nthawiyo, adzaphedwa ndi lupanga.+
15 Aliyense amene adzapezedwe adzabooledwa ndipo aliyense amene adzagwidwe limodzi ndi anthu ena onse pa nthawiyo, adzaphedwa ndi lupanga.+