Yesaya 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma iweyo watayidwa popanda kuikidwa m’manda,+ ngati mphukira yonyansa imene ili pakati pa anthu akufa ophedwa ndi lupanga, amene akutsikira kumiyala ya m’dzenje.+ Watayidwa ngati mtembo wopondedwapondedwa.+ Yeremiya 50:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iphani ng’ombe zake zonse zazing’ono zamphongo.+ Zonse zipite kokaphedwa.+ Tsoka kwa iwo, chifukwa tsiku lawo lafika. Nthawi yoti alangidwe yafika.+ Yeremiya 51:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Munthu wodziwa kukunga uta musamulole kuchita zimenezo.+ Musamulole kunyamuka kuti amenye nkhondo atavala chovala chamamba achitsulo. “Anthu inu musamvere chisoni anyamata ake.+ Wonongani gulu lake lonse la asilikali.+
19 Koma iweyo watayidwa popanda kuikidwa m’manda,+ ngati mphukira yonyansa imene ili pakati pa anthu akufa ophedwa ndi lupanga, amene akutsikira kumiyala ya m’dzenje.+ Watayidwa ngati mtembo wopondedwapondedwa.+
27 Iphani ng’ombe zake zonse zazing’ono zamphongo.+ Zonse zipite kokaphedwa.+ Tsoka kwa iwo, chifukwa tsiku lawo lafika. Nthawi yoti alangidwe yafika.+
3 “Munthu wodziwa kukunga uta musamulole kuchita zimenezo.+ Musamulole kunyamuka kuti amenye nkhondo atavala chovala chamamba achitsulo. “Anthu inu musamvere chisoni anyamata ake.+ Wonongani gulu lake lonse la asilikali.+