2 Mafumu 9:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Atapita kuti akam’tenge kukamuika m’manda, sanapezepo chilichonse. Iwo anangopezapo mutu, mapazi, ndi zikhatho zake. + Yeremiya 22:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Adzaikidwa m’manda ngati mmene amaikira bulu wamphongo.+ Adzamukoka kudutsa naye pazipata za Yerusalemu ndi kukamutaya kunja.’+
35 Atapita kuti akam’tenge kukamuika m’manda, sanapezepo chilichonse. Iwo anangopezapo mutu, mapazi, ndi zikhatho zake. +
19 Adzaikidwa m’manda ngati mmene amaikira bulu wamphongo.+ Adzamukoka kudutsa naye pazipata za Yerusalemu ndi kukamutaya kunja.’+