2 Mafumu 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yezebeli adzadyedwa ndi agalu+ m’munda wa ku Yezereeli, ndipo palibe amene adzamuike m’manda.’” Mtumikiyo atamaliza kunena zimenezi, anatsegula chitseko n’kuthawa.+ Yesaya 14:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Sudzakhalira nawo limodzi m’manda, chifukwa unawononga dziko lako lomwe, ndipo unapha anthu ako omwe. Mayina a ana a anthu ochita zoipa sadzatchulidwanso mpaka kalekale.+ Yeremiya 22:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Adzaikidwa m’manda ngati mmene amaikira bulu wamphongo.+ Adzamukoka kudutsa naye pazipata za Yerusalemu ndi kukamutaya kunja.’+
10 Yezebeli adzadyedwa ndi agalu+ m’munda wa ku Yezereeli, ndipo palibe amene adzamuike m’manda.’” Mtumikiyo atamaliza kunena zimenezi, anatsegula chitseko n’kuthawa.+
20 Sudzakhalira nawo limodzi m’manda, chifukwa unawononga dziko lako lomwe, ndipo unapha anthu ako omwe. Mayina a ana a anthu ochita zoipa sadzatchulidwanso mpaka kalekale.+
19 Adzaikidwa m’manda ngati mmene amaikira bulu wamphongo.+ Adzamukoka kudutsa naye pazipata za Yerusalemu ndi kukamutaya kunja.’+