Yobu 18:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pansi, mizu yake idzauma.+Pamwamba, nthambi yake idzafota. Salimo 21:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mudzawononga ana awo kuwachotsa padziko lapansi,+Ndipo ana awo mudzawachotsa pakati pa ana a anthu.+ Salimo 37:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pakuti Yehova amakonda chilungamo,+Ndipo sadzasiya anthu ake okhulupirika.+ ע [ʽAʹyin]Adzawateteza mpaka kalekale.+Koma ana a anthu oipa adzaphedwa.+ Salimo 109:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mbadwa zake ziphedwe ndi kuchotsedwa m’dziko.+Dzina lawo lifafanizidwe mu m’badwo wotsatira.+ Salimo 137:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwe mwana wamkazi wa Babulo, amene udzafunkhidwa,+Wodala ndi amene adzakubwezera+Zimene iwe watichitira.+
10 Mudzawononga ana awo kuwachotsa padziko lapansi,+Ndipo ana awo mudzawachotsa pakati pa ana a anthu.+
28 Pakuti Yehova amakonda chilungamo,+Ndipo sadzasiya anthu ake okhulupirika.+ ע [ʽAʹyin]Adzawateteza mpaka kalekale.+Koma ana a anthu oipa adzaphedwa.+
8 Iwe mwana wamkazi wa Babulo, amene udzafunkhidwa,+Wodala ndi amene adzakubwezera+Zimene iwe watichitira.+